Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,

      Kasupe wa Yakobo adzakhala motetezeka,

      Mʼdziko lokhala ndi chakudya komanso vinyo watsopano,+

      Limene kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+

  • Yeremiya 32:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 ‘Ine ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko onse kumene ndinawabalalitsira nditakwiya, kupsa mtima ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+ Ndidzawabwezeretsa mʼdziko lino nʼkuwachititsa kuti azikhala motetezeka.+

  • Zekariya 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anthu adzakhala mumzindawo ndipo sudzatembereredwanso kuti uwonongedwe.+ Anthu azidzakhala mu Yerusalemu motetezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena