Yesaya 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dzikolo likulira*+ ndipo likuwonongeka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo ikutha. Anthu otchuka amʼdzikolo afota. Yoweli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munda wawonongedwa ndipo nthaka ikulira.+Mbewu zawonongedwa, vinyo watsopano watha ndipo mafuta sakupezekanso.+
4 Dzikolo likulira*+ ndipo likuwonongeka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo ikutha. Anthu otchuka amʼdzikolo afota.
10 Munda wawonongedwa ndipo nthaka ikulira.+Mbewu zawonongedwa, vinyo watsopano watha ndipo mafuta sakupezekanso.+