Ezekieli 16:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Mkulu wako ndi Samariya+ amene akukhala kumpoto kwako* limodzi ndi ana ake aakazi.*+ Ndipo mngʼono wako ndi Sodomu,+ amene akukhala kumʼmwera kwako* limodzi ndi ana ake aakazi.+
46 Mkulu wako ndi Samariya+ amene akukhala kumpoto kwako* limodzi ndi ana ake aakazi.*+ Ndipo mngʼono wako ndi Sodomu,+ amene akukhala kumʼmwera kwako* limodzi ndi ana ake aakazi.+