Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kenako Yehova anati: “Ndamva madandaulo ambiri+ akuti machimo a anthu amene akukhala mʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora ndi oipa kwambiri.+

  • Deuteronomo 32:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mtengo wawo wa mpesa ndi wochokera ku mtengo wa mpesa wa ku Sodomu,

      Ndi kuminda ya mʼmapiri a ku Gomora.+

      Zipatso zawo za mphesa ndi zapoizoni

      Ndipo ndi zowawa.+

  • Yesaya 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Imvani mawu a Yehova, inu olamulira ankhanza a ku Sodomu.+

      Mvetserani malamulo* a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.+

  • Yuda 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mofanana ndi zimenezi, anthu amʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora komanso mizinda yozungulira ankachita chiwerewere* chonyansa kwambiri ndiponso kugonana mʼnjira imene si yachibadwa.+ Anthu amenewa anapatsidwa chilango cha chiwonongeko chosatha*+ ndipo ndi chitsanzo chotichenjeza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena