Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Nʼchifukwa chiyani tikungokhala pano?

      Tiyeni tisonkhane pamodzi ndipo tilowe mʼmizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri+ kuti tikafere kumeneko.

      Chifukwa Yehova Mulungu wathu adzatiwononga,

      Ndipo amatipatsa madzi apoizoni kuti timwe,+

      Chifukwa tachimwira Yehova.

  • Yeremiya 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndidzadyetsa anthu amenewa chitsamba chowawa ndipo ndidzawamwetsa madzi apoizoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena