-
Yeremiya 25:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse omwe anali aneneri. Ankawatumiza mobwerezabwereza* koma inu simunawamvere kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+ 5 Iwo ankakuuzani kuti, ‘Chonde, aliyense wa inu atembenuke nʼkusiya njira zake zoipa ndi zochita zake zoipa.+ Mukatero mudzapitiriza kukhala kwa nthawi yaitali mʼdziko limene Yehova anakupatsani kalekale, inuyo ndi makolo anu.
-