Zefaniya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aneneri ake ndi amwano ndiponso achinyengo.+ Ansembe ake amaipitsa zinthu zopatulika,+Ndipo amaphwanya malamulo.+
4 Aneneri ake ndi amwano ndiponso achinyengo.+ Ansembe ake amaipitsa zinthu zopatulika,+Ndipo amaphwanya malamulo.+