Yeremiya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma inu mukukhulupirira mawu achinyengo+ ndipo sakuthandizani ngakhale pangʼono. Maliro 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Masomphenya amene aneneri anu anaona ndi abodza komanso achabechabe,+Ndipo sanaulule zolakwa zanu nʼcholinga choti musatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma ankaona masomphenya abodza komanso okusocheretsani.+
14 Masomphenya amene aneneri anu anaona ndi abodza komanso achabechabe,+Ndipo sanaulule zolakwa zanu nʼcholinga choti musatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma ankaona masomphenya abodza komanso okusocheretsani.+