2 Mafumu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Yehoyakimu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira+ ndipo mwana wake Yehoyakini anakhala mfumu mʼmalo mwake. 1 Mbiri 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwana wa Yehoyakimu+ anali Yekoniya. Yekoniya anabereka Zedekiya.
6 Kenako Yehoyakimu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira+ ndipo mwana wake Yehoyakini anakhala mfumu mʼmalo mwake.