Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Aliyense amene ali pakati panu mwa anthu onse amene amamutumikira, Mulungu wake akhale naye ndipo apite ku Yerusalemu mʼdziko la Yuda nʼkukamanganso nyumba ya Yehova Mulungu wa Isiraeli. Iye ndi Mulungu woona ndipo nyumba yake inali ku Yerusalemu.*

  • Yeremiya 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma ndikadzawazula, ndidzawachitiranso chifundo moti ndidzabwezeretsa aliyense wa iwo pacholowa chake ndi pamalo ake.

  • Yeremiya 25:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja ndipo lidzakhala chinthu chochititsa mantha. Mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+

  • Yeremiya 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Yehova wanena kuti, ‘Zaka 70 zikadzakwana muli ku Babulo, ndidzakusamalirani+ ndipo ndidzakwaniritsa lonjezo langa pokubwezeretsani kumalo ano.’+

  • Ezekieli 36:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 ‘Ndidzakutengani kuchokera kwa anthu a mitundu ina nʼkukusonkhanitsani pamodzi kuchokera mʼmayiko onse ndipo ndidzakubwezeretsani mʼdziko lanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena