Yeremiya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Taona, lero ndakupatsa mphamvu pa mitundu ya anthu ndi maufumu, kuti uzule ndi kugwetsa, uwononge ndi kupasula, komanso kuti umange ndi kudzala.”+ Yeremiya 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova wanena kuti: “Ndikusonkhanitsa anthu amʼmatenti a Yakobo amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,+Ndipo ndidzamvera chisoni malo okhala a Yakobo. Mzinda udzamangidwanso pamalo amene unali poyamba,+Ndipo nsanja yokhala ndi mpanda wolimba idzakhala pamalo ake oyenerera. Yeremiya 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndidzasangalala nawo ndipo ndidzawachitira zabwino.+ Ndidzawachititsa kuti azikhala mʼdziko lino+ mpaka kalekale. Ndidzachita zimenezi ndi mtima wanga wonse komanso moyo wanga wonse.’”
10 Taona, lero ndakupatsa mphamvu pa mitundu ya anthu ndi maufumu, kuti uzule ndi kugwetsa, uwononge ndi kupasula, komanso kuti umange ndi kudzala.”+
18 Yehova wanena kuti: “Ndikusonkhanitsa anthu amʼmatenti a Yakobo amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,+Ndipo ndidzamvera chisoni malo okhala a Yakobo. Mzinda udzamangidwanso pamalo amene unali poyamba,+Ndipo nsanja yokhala ndi mpanda wolimba idzakhala pamalo ake oyenerera.
41 Ndidzasangalala nawo ndipo ndidzawachitira zabwino.+ Ndidzawachititsa kuti azikhala mʼdziko lino+ mpaka kalekale. Ndidzachita zimenezi ndi mtima wanga wonse komanso moyo wanga wonse.’”