Yeremiya 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘Mudzandifunafuna ndipo mudzandipeza+ chifukwa mudzandifunafuna ndi mtima wanu wonse.+