-
Yeremiya 27:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ukatero, uwalamule kuti akauze ambuye awo kuti:
“Mukauze ambuye anu kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti,
-
-
Yeremiya 27:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 ‘Ngati mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu udzakane kutumikira Mfumu Nebukadinezara ya ku Babulo komanso kukana kuika khosi lake mʼgoli la mfumu ya Babulo, ine ndidzalanga mtundu umenewo ndi lupanga,+ njala komanso mliri* mpaka nditauwononga wonse pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadinezara,’ akutero Yehova.
-