2 Mafumu 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehoyakimu+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 25 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya. 2 Mafumu 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Yehoyakimu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira+ ndipo mwana wake Yehoyakini anakhala mfumu mʼmalo mwake.
36 Yehoyakimu+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 25 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya.
6 Kenako Yehoyakimu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira+ ndipo mwana wake Yehoyakini anakhala mfumu mʼmalo mwake.