Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani. Yeremiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye akadzafunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova Mulungu wathu watichitira zinthu zonsezi?’ udzawayankhe kuti, ‘Mofanana ndi mmene munandisiyira nʼkukatumikira mulungu wachilendo mʼdziko lanu, mudzatumikiranso alendo mʼdziko limene si lanu.’”+
48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani.
19 Ndiye akadzafunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova Mulungu wathu watichitira zinthu zonsezi?’ udzawayankhe kuti, ‘Mofanana ndi mmene munandisiyira nʼkukatumikira mulungu wachilendo mʼdziko lanu, mudzatumikiranso alendo mʼdziko limene si lanu.’”+