Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 49:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma Yehova akunena kuti:

      “Ngakhale anthu amene agwidwa ndi munthu wamphamvu adzalandidwa,+

      Ndipo amene anagwidwa ndi wolamulira wankhanza adzapulumutsidwa.+

      Ndidzalimbana ndi aliyense amene akulimbana nawe,+

      Ndipo ana ako ndidzawapulumutsa.

  • Yeremiya 30:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Taona! masiku akubwera,” akutero Yehova, “pamene ndidzasonkhanitsa Isiraeli ndi Yuda,+ anthu anga amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,” akutero Yehova. “Iwo ndidzawabwezeretsa kudziko limene ndinapatsa makolo awo ndipo adzalitenga kuti likhalenso lawo.”’”+

  • Ezekieli 39:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 ‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa ku ukapolo pakati pa anthu a mitundu ina, kenako nʼkuwabwezeretsa kudziko lawo osasiyako wina aliyense.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena