Yesaya 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Malo ouma chifukwa cha kutentha adzakhala dambo la madzi,Ndipo malo aludzu adzakhala ndi akasupe amadzi.+ Mʼmalo amene mimbulu inkakhala,+Mudzakhala udzu wobiriwira, bango ndi gumbwa.* Yesaya 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sadzakhala ndi njala ndipo sadzamva ludzu,+Komanso sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Chifukwa amene amawachitira chifundo adzawatsogolera+Ndipo adzapita nawo kumene kuli akasupe amadzi.+
7 Malo ouma chifukwa cha kutentha adzakhala dambo la madzi,Ndipo malo aludzu adzakhala ndi akasupe amadzi.+ Mʼmalo amene mimbulu inkakhala,+Mudzakhala udzu wobiriwira, bango ndi gumbwa.*
10 Iwo sadzakhala ndi njala ndipo sadzamva ludzu,+Komanso sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Chifukwa amene amawachitira chifundo adzawatsogolera+Ndipo adzapita nawo kumene kuli akasupe amadzi.+