Aheberi 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Pangano limene ndidzapangane nawo pambuyo pa masiku amenewo ndi ili: Ndidzaika malamulo anga mʼmitima yawo ndipo ndidzawalemba mʼmaganizo awo,’+ akutero Yehova.”*
16 “‘Pangano limene ndidzapangane nawo pambuyo pa masiku amenewo ndi ili: Ndidzaika malamulo anga mʼmitima yawo ndipo ndidzawalemba mʼmaganizo awo,’+ akutero Yehova.”*