Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Yehova ndi gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa+ komanso kapu yanga.+

      Inu mumateteza cholowa changa.

  • Salimo 73:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Thupi langa ndi mtima wanga zingalefuke,

      Koma Mulungu ndi thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+

  • Salimo 142:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndikuitana inu Yehova kuti mundithandize.

      Ndikunena kuti: “Inu ndinu malo anga othawirako,+

      Malo okhawo amene ndili nawo* mʼdziko la anthu amoyo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena