Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndithudi, palibe anthu amene amayembekezera inu amene adzachite manyazi.+

      Koma amene adzachite manyazi ndi anthu amene amachita zachinyengo popanda chifukwa.+

  • Salimo 130:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndikuyembekezera Yehova. Moyo wanga wonse ukumuyembekezera.

      Ine ndikuyembekezera mawu ake.

  • Yesaya 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pa tsiku limenelo anthu akewo adzanena kuti:

      “Taonani! Uyu ndi Mulungu wathu.+

      Chiyembekezo chathu chinali mwa iye+

      Ndipo iye watipulumutsa.+

      Uyu ndi Yehova.

      Chiyembekezo chathu chinali mwa iye.

      Tiyeni tisangalale ndi kukondwera chifukwa watipulumutsa.”+

  • Yesaya 30:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma Yehova akuyembekezera moleza mtima kuti akukomereni mtima,+

      Ndipo adzanyamuka kuti akuchitireni chifundo,+

      Chifukwa Yehova ndi Mulungu amene amaweruza mwachilungamo.+

      Osangalala ndi anthu onse amene akumuyembekezera.+

  • Mika 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Koma ine ndidzayembekezera Yehova.+

      Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+

      Mulungu wanga adzandimvera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena