3 Zimenezi zinachitikira Ayuda molamulidwa ndi Yehova, kuti awachotse pamaso pake+ chifukwa cha machimo onse amene Manase anachita+ 4 komanso chifukwa cha anthu ambiri osalakwa amene anawapha,+ moti anadzaza Yerusalemu ndi magazi a anthu osalakwa ndipo Yehova sanafune kukhululuka.+