Yesaya 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinthu ziwiri izi zakugwera. Ndi ndani amene akumvere chisoni? Kuwonongedwa ndi kusakazidwa, njala ndi lupanga!+ Kodi ndi ndani amene akutonthoze?+ Yeremiya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kwezani chizindikiro choloza njira ya ku Ziyoni. Thawirani kumalo otetezeka, musangoima,” Chifukwa ndikubweretsa tsoka kuchokera kumpoto,+ tsoka lalikulu kwambiri.
19 Zinthu ziwiri izi zakugwera. Ndi ndani amene akumvere chisoni? Kuwonongedwa ndi kusakazidwa, njala ndi lupanga!+ Kodi ndi ndani amene akutonthoze?+
6 Kwezani chizindikiro choloza njira ya ku Ziyoni. Thawirani kumalo otetezeka, musangoima,” Chifukwa ndikubweretsa tsoka kuchokera kumpoto,+ tsoka lalikulu kwambiri.