Ezekieli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsiku lililonse uzidzadya chakudya chochita kuyeza. Uzidzadya chakudya chokwana masekeli 20.* Uzidzadya chakudyachi nthawi yofanana tsiku lililonse.
10 Tsiku lililonse uzidzadya chakudya chochita kuyeza. Uzidzadya chakudya chokwana masekeli 20.* Uzidzadya chakudyachi nthawi yofanana tsiku lililonse.