2 Mafumu 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼmwezi wa 4, pa tsiku la 9, njala inafika poipa kwambiri+ mumzindawo ndipo anthu analibiretu chakudya.+ Maliro 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala.Anthu sakuthanso kuwazindikira mʼmisewu. Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo wouma.
3 Mʼmwezi wa 4, pa tsiku la 9, njala inafika poipa kwambiri+ mumzindawo ndipo anthu analibiretu chakudya.+
8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala.Anthu sakuthanso kuwazindikira mʼmisewu. Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo wouma.