Yeremiya 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala mʼmalowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale.
10 Ndidzathetsa phokoso lachikondwerero ndi phokoso lakusangalala mʼmalowo.+ Ndidzathetsanso mawu osangalala a mkwati ndi a mkwatibwi.+ Simudzamvekanso kupera kwa mphero ndipo simudzaonekanso kuwala kwa nyale.