Deuteronomo 28:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Mudzasowa mtendere pakati pa mitundu imeneyo,+ ndipo simudzapeza malo oti phazi lanu liponde kuti lipume. Mʼmalomwake, Yehova adzakupatsani mtima wankhawa,+ adzachititsa kuti maso anu aziona movutikira ndipo adzakuchititsani kuti mutaye mtima.+
65 Mudzasowa mtendere pakati pa mitundu imeneyo,+ ndipo simudzapeza malo oti phazi lanu liponde kuti lipume. Mʼmalomwake, Yehova adzakupatsani mtima wankhawa,+ adzachititsa kuti maso anu aziona movutikira ndipo adzakuchititsani kuti mutaye mtima.+