Salimo 102:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma inu Yehova, mudzakhalapobe kwamuyaya,+Dzina lanu lidzakhalapobe* ku mibadwo yonse.+ Salimo 145:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ufumu wanu ndi ufumu wamuyaya,Ndipo ulamuliro wanu udzakhalapo ku mibadwo yonse.+ Salimo 146:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzakhala Mfumu kwamuyaya,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala Mfumu ku mibadwomibadwo. Tamandani Ya!*
10 Yehova adzakhala Mfumu kwamuyaya,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala Mfumu ku mibadwomibadwo. Tamandani Ya!*