Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoweli 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma Iguputo adzasanduka bwinja,+

      Ndipo Edomu adzakhala chipululu chopanda kanthu.+

      Chifukwa cha nkhanza zimene anachitira anthu a ku Yuda,+

      Ndiponso chifukwa chokhetsa magazi a anthu osalakwa mʼdziko la Yudalo.+

  • Malaki 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Esau ndinadana naye.+ Mapiri ake ndinawasandutsa bwinja+ ndipo cholowa chake ndinachisandutsa malo okhala mimbulu yamʼchipululu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena