Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+ Obadiya 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza unachitira nkhanza mʼbale wako Yakobo,+Udzachititsidwa manyazi kwambiri.+Udzaphedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.+
7 Inu Yehova, kumbukiraniZimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa. Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+
10 Popeza unachitira nkhanza mʼbale wako Yakobo,+Udzachititsidwa manyazi kwambiri.+Udzaphedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.+