Maliro 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kondwa ndipo usangalale, iwe mwana wamkazi wa Edomu,+ amene ukukhala mʼdziko la Uzi. Koma iwenso kapu ya tsoka idzakupeza.+ Udzaledzera ndipo udzavula nʼkukhala maliseche.+ Obadiya 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwe sumayenera kunyadira pa tsiku limene mʼbale wako anakumana ndi tsoka,+Sumayenera kusangalala pa tsiku limene anthu a ku Yuda ankawonongedwa,+Sumayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene ankazunzika. Obadiya 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku la Yehova limene adzalange mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Zimene wachitira mʼbale wako, iwenso adzakuchitira zomwezo.+ Zimene unachitira anthu ena zidzakubwerera pamutu pako.
21 Kondwa ndipo usangalale, iwe mwana wamkazi wa Edomu,+ amene ukukhala mʼdziko la Uzi. Koma iwenso kapu ya tsoka idzakupeza.+ Udzaledzera ndipo udzavula nʼkukhala maliseche.+
12 Iwe sumayenera kunyadira pa tsiku limene mʼbale wako anakumana ndi tsoka,+Sumayenera kusangalala pa tsiku limene anthu a ku Yuda ankawonongedwa,+Sumayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene ankazunzika.
15 Tsiku la Yehova limene adzalange mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Zimene wachitira mʼbale wako, iwenso adzakuchitira zomwezo.+ Zimene unachitira anthu ena zidzakubwerera pamutu pako.