Salimo 79:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu oyandikana nafe akutinyoza,+Anthu otizungulira akutiseka komanso kutikuwiza. Ezekieli 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu a mitundu ina sadzawagwiranso ndipo zilombo zolusa sizidzawadya. Iwo azidzakhala motetezeka popanda aliyense wowaopseza.+
28 Anthu a mitundu ina sadzawagwiranso ndipo zilombo zolusa sizidzawadya. Iwo azidzakhala motetezeka popanda aliyense wowaopseza.+