Ezekieli 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndidzawapatsa munda umene udzakhale wotchuka* chifukwa cha mbewu zake ndipo anthu sadzafanso ndi njala mʼdzikomo+ komanso anthu a mitundu ina sadzawanyozanso.+
29 Ndidzawapatsa munda umene udzakhale wotchuka* chifukwa cha mbewu zake ndipo anthu sadzafanso ndi njala mʼdzikomo+ komanso anthu a mitundu ina sadzawanyozanso.+