Ezekieli 34:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mitengo yamʼdzikomo idzabereka zipatso ndipo nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala mʼdzikolo motetezeka ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzathyola goli lawo+ nʼkuwapulumutsa kwa anthu amene anawagwira kuti akhale akapolo awo.
27 Mitengo yamʼdzikomo idzabereka zipatso ndipo nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala mʼdzikolo motetezeka ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzathyola goli lawo+ nʼkuwapulumutsa kwa anthu amene anawagwira kuti akhale akapolo awo.