Ezekieli 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Adzakhala mʼdzikolo motetezeka+ ndipo adzamanga nyumba komanso kulima minda ya mpesa.+ Iwo azidzakhala motetezeka ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene amawanyoza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’” Ezekieli 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu ndipo mudzakhala amoyo.+ Ndidzakukhazikani mʼdziko lanu ndipo mudzadziwa kuti ine Yehova ndinanena zimenezi ndipo ndazichita,’ akutero Yehova.”
26 Adzakhala mʼdzikolo motetezeka+ ndipo adzamanga nyumba komanso kulima minda ya mpesa.+ Iwo azidzakhala motetezeka ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene amawanyoza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’”
14 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu ndipo mudzakhala amoyo.+ Ndidzakukhazikani mʼdziko lanu ndipo mudzadziwa kuti ine Yehova ndinanena zimenezi ndipo ndazichita,’ akutero Yehova.”