-
Ezekieli 8:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kenako iye anatambasula chinachake chooneka ngati dzanja ndipo anagwira tsitsi lakumutu kwanga nʼkundinyamula. Ndiyeno mzimu unandinyamulira mʼmalere pakati pa dziko lapansi ndi kumwamba, nʼkundipititsa ku Yerusalemu mʼmasomphenya ochokera kwa Mulungu. Mzimuwo unandifikitsa pakhomo la geti la bwalo lamkati+ loyangʼana kumpoto pamene panali fano loimira nsanje, limene limachititsa nsanje.+
-