Yesaya 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmasiku otsiriza,Phiri la nyumba ya YehovaLidzakhazikika pamwamba penipeni pa mapiri akuluakulu,+Ndipo lidzakwezedwa kupitirira mapiri angʼonoangʼono.Anthu a mitundu yonse adzapita kumeneko.+
2 Mʼmasiku otsiriza,Phiri la nyumba ya YehovaLidzakhazikika pamwamba penipeni pa mapiri akuluakulu,+Ndipo lidzakwezedwa kupitirira mapiri angʼonoangʼono.Anthu a mitundu yonse adzapita kumeneko.+