Ezekieli 43:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwe mwana wa munthu, ufotokozere nyumba ya Isiraeli za kachisiyu+ kuti achite manyazi chifukwa cha zolakwa zawo,+ ndipo iwo aonetsetse pulani ya kachisiyu* kuti adziwe mmene anamangidwira.
10 Koma iwe mwana wa munthu, ufotokozere nyumba ya Isiraeli za kachisiyu+ kuti achite manyazi chifukwa cha zolakwa zawo,+ ndipo iwo aonetsetse pulani ya kachisiyu* kuti adziwe mmene anamangidwira.