Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 9:26, 27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pamagetiwo panali akuluakulu 4 oyangʼanira amene anaikidwa pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo. Iwo anali Alevi ndipo ankayangʼanira zipinda zodyera ndi chuma chamʼnyumba ya Mulungu woona.+ 27 Usiku ankakhala mʼmalo awo mozungulira nyumba yonse ya Mulungu woona chifukwa ankachita utumiki wawo waulonda. Iwowa ndi amene ankasunga makiyi nʼkumatsegula nyumbayo mʼmawa uliwonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena