Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 40:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Bwalo lakunja linali ndi kanyumba kapageti kamene kanayangʼana kumpoto. Iye anayeza mulitali ndi mulifupi mwake. 21 Kanyumba kapagetiko kanali ndi zipinda zitatu za alonda mbali iliyonse. Miyezo ya zipilala zake zamʼmbali komanso khonde lake, inali yofanana ndi ya kanyumba kapageti koyamba kaja. Kanyumbako kanali mikono 50 mulitali ndi mikono 25 mulifupi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena