-
Ezekieli 46:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Anthu amʼdzikoli akafika pamaso pa Yehova pa nthawi ya zikondwerero,+ anthu amene alowa kudzalambira kudzera pageti la kumpoto+ azidzatulukira pageti lakumʼmwera.+ Amene alowera pageti lakumʼmwera azidzatulukira pageti lakumpoto. Munthu aliyense asadzatulukire pageti limene analowera chifukwa aliyense akuyenera kutulukira pageti limene lili kutsogolo kwake.
-