Ezekieli 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anandipititsa kutsogolo kwa kachisi kudzera pageti lakumpoto. Nditayangʼana ndinaona kuti ulemerero wa Yehova wadzaza mʼkachisi wa Yehova.+ Choncho ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+
4 Kenako anandipititsa kutsogolo kwa kachisi kudzera pageti lakumpoto. Nditayangʼana ndinaona kuti ulemerero wa Yehova wadzaza mʼkachisi wa Yehova.+ Choncho ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+