Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati akupereka ngʼombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyama ya nsembe yopserezayo aziisenda nʼkuiduladula.+ Levitiko 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anaduladula nkhosayo ndipo Mose anatenga mutu wake, nyama yoduladulayo ndi mafuta ake,* nʼkuziwotcha. Ezekieli 43:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena kuti: ‘Amenewa ndi malangizo amene akuyenera kutsatiridwa popanga guwa lansembe kuti aziperekerapo nsembe zopsereza zathunthu ndi kuwazapo magazi.+
3 Ngati akupereka ngʼombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza, azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
20 Anaduladula nkhosayo ndipo Mose anatenga mutu wake, nyama yoduladulayo ndi mafuta ake,* nʼkuziwotcha.
18 Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti, “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena kuti: ‘Amenewa ndi malangizo amene akuyenera kutsatiridwa popanga guwa lansembe kuti aziperekerapo nsembe zopsereza zathunthu ndi kuwazapo magazi.+