Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Azibweretsanso kwa Yehova nsembe yake yakupalamula chifukwa cha tchimo limene wachita.+ Azibweretsa nkhosa yaingʼono yaikazi kapena mbuzi yaingʼono yaikazi kuti ikhale nsembe yamachimo. Akatero wansembe aziphimba tchimo la munthuyo.

  • Levitiko 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Lamulo la nsembe yakupalamula+ ndi ili: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.

  • Ezekieli 42:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti: “Nyumba zodyera zakumpoto ndi zakumʼmwera zimene zili pafupi ndi malo opanda kanthu,+ ndi nyumba zodyera zopatulika, kumene ansembe otumikira Yehova amadyerako nsembe zopatulika koposa.+ Mʼnyumbazo amaikamo nsembe zopatulika koposa zomwe ndi nsembe zambewu, nsembe zamachimo ndi nsembe zakupalamula, chifukwa malo amenewa ndi oyera.+

  • Ezekieli 44:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iwowa ndi amene azidzadya nsembe yambewu,+ nsembe yamachimo ndi nsembe yakupalamula+ ndipo chilichonse choperekedwa kwa Mulungu mu Isiraeli chidzakhala chawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena