Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mikango yamphamvu* yamubangulira.+

      Yamutulutsira mawu amphamvu.

      Yachititsa kuti dziko lake likhale chinthu chochititsa mantha.

      Mizinda yake aiyatsa moto, moti simukukhalanso munthu aliyense.

  • Yeremiya 32:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Akasidi amene akumenyana ndi anthu amumzindawu adzabwera nʼkuyatsa mzindawu moti udzapseratu.+ Adzawotchanso nyumba zimene pamadenga ake anthu ankaperekerapo nsembe kwa Baala komanso nsembe zachakumwa kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.’+

  • Mika 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Choncho chifukwa cha anthu inu,

      Ziyoni adzalimidwa ngati munda,

      Yerusalemu adzakhala mabwinja.+

      Ndipo phiri la nyumba* ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena