1 Mafumu 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chipinda chamʼmbali chapansi chinali mikono 5 mulifupi mwake, chapakati chinali mikono 6 mulifupi mwake ndipo chachitatu chinali mikono 7 mulifupi mwake. Makoma onse akunja a nyumbayo anangowagoba nʼcholinga choti asawaboole.+ 1 Mafumu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anamanga zipinda zamʼmbali zosanjikizana kuzungulira nyumbayo+ ndipo chipinda chilichonse chinali chachitali mikono 5. Zipindazo anazilumikiza kunyumbayo ndi matabwa a mkungudza.
6 Chipinda chamʼmbali chapansi chinali mikono 5 mulifupi mwake, chapakati chinali mikono 6 mulifupi mwake ndipo chachitatu chinali mikono 7 mulifupi mwake. Makoma onse akunja a nyumbayo anangowagoba nʼcholinga choti asawaboole.+
10 Anamanga zipinda zamʼmbali zosanjikizana kuzungulira nyumbayo+ ndipo chipinda chilichonse chinali chachitali mikono 5. Zipindazo anazilumikiza kunyumbayo ndi matabwa a mkungudza.