1 Mafumu 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamakoma onse a nyumbayo a zipinda zonse ziwiri, zomwe ndi Malo Oyera Koposa komanso Malo Oyera, anajambulapo mochita kugoba akerubi,+ mitengo ya kanjedza+ ndi maluwa.+ 1 Mafumu 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Patimafelemuto ndiponso pamalata amʼmbaliwo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mikango komanso mitengo ya kanjedza mogwirizana ndi kukula kwa malo ake. Anajambulanso nkhata zamaluwa kuzungulira chokhazikapo besenicho.+ 2 Mbiri 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo matabwa ake akudenga, pamakomo, makoma ndi zitseko za nyumbayo anazikuta ndi golide.+ Pamakoma ake anajambulapo akerubi mochita kugoba.+
29 Pamakoma onse a nyumbayo a zipinda zonse ziwiri, zomwe ndi Malo Oyera Koposa komanso Malo Oyera, anajambulapo mochita kugoba akerubi,+ mitengo ya kanjedza+ ndi maluwa.+
36 Patimafelemuto ndiponso pamalata amʼmbaliwo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mikango komanso mitengo ya kanjedza mogwirizana ndi kukula kwa malo ake. Anajambulanso nkhata zamaluwa kuzungulira chokhazikapo besenicho.+
7 Ndipo matabwa ake akudenga, pamakomo, makoma ndi zitseko za nyumbayo anazikuta ndi golide.+ Pamakoma ake anajambulapo akerubi mochita kugoba.+