Ezekieli 44:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Iwo ndi amene adzalowe mʼmalo anga opatulika. Adzayandikira tebulo langa kuti anditumikire+ ndipo adzagwira ntchito zimene apatsidwa ponditumikira.+ Malaki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Mwalinyoza popereka nsembe* zodetsedwa paguwa langa lansembe.’ ‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani bwanji?”’ ‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo la Yehova+ ndi lonyozeka.”
16 ‘Iwo ndi amene adzalowe mʼmalo anga opatulika. Adzayandikira tebulo langa kuti anditumikire+ ndipo adzagwira ntchito zimene apatsidwa ponditumikira.+
7 ‘Mwalinyoza popereka nsembe* zodetsedwa paguwa langa lansembe.’ ‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani bwanji?”’ ‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo la Yehova+ ndi lonyozeka.”