Salimo 78:40, 41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Nthawi zambiri iwo ankamupandukira mʼchipululu,+Ndipo ankamukhumudwitsa mʼchipululumo!+ 41 Ankayesa Mulungu mobwerezabwereza,+Ndipo ankachititsa kuti Woyera wa Isiraeli amve chisoni.* Yesaya 63:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo anapanduka+ nʼkumvetsa chisoni mzimu wake woyera.+ Kenako iye anakhala mdani wawo,+Ndipo anachita nawo nkhondo.+
40 Nthawi zambiri iwo ankamupandukira mʼchipululu,+Ndipo ankamukhumudwitsa mʼchipululumo!+ 41 Ankayesa Mulungu mobwerezabwereza,+Ndipo ankachititsa kuti Woyera wa Isiraeli amve chisoni.*
10 Koma iwo anapanduka+ nʼkumvetsa chisoni mzimu wake woyera.+ Kenako iye anakhala mdani wawo,+Ndipo anachita nawo nkhondo.+