Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno akakufunsa kuti, ‘Tipite kuti?’ uwayankhe kuti, ‘Yehova wanena kuti:

      “Amene akuyenera kufa ndi mliri afe ndi mliri!

      Amene akuyenera kufa ndi lupanga afe ndi lupanga!+

      Amene akuyenera kufa ndi njala yaikulu afe ndi njala yaikulu!

      Amene akuyenera kutengedwa kupita ku ukapolo atengedwe kupita ku ukapolo!”’+

  • Yeremiya 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ‘Iwo adzafa ndi matenda oopsa+ koma palibe amene adzalire maliro awo kapena kuwaika mʼmanda. Iwo adzakhala ngati manyowa panthaka.+ Adzafa ndi lupanga ndiponso njala.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha mbalame zamumlengalenga ndi zilombo zakutchire.’

  • Ezekieli 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Gawo limodzi la magawo atatu a anthu a mtundu wako lidzafa ndi mliri* kapena lidzafa ndi njala pakati pako. Gawo lina lidzaphedwa ndi lupanga mokuzungulira.+ Gawo lachitatu ndidzalibalalitsira kumbali zonse, ndipo ndidzalithamangitsa nditasolola lupanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena