Yobu 39:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kapena kodi chiwombankhanga chimauluka mʼmwamba chifukwa choti iweyo wachilamula,+Nʼkukamanga chisa chake pamwamba kwambiri?+ Yobu 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chili pamalo omwewo, chimafunafuna chakudya,+Maso ake amaona kutali kwambiri.
27 Kapena kodi chiwombankhanga chimauluka mʼmwamba chifukwa choti iweyo wachilamula,+Nʼkukamanga chisa chake pamwamba kwambiri?+ Yobu 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chili pamalo omwewo, chimafunafuna chakudya,+Maso ake amaona kutali kwambiri.